Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Nyimbo Ya Chikondi

๐Ÿ‘ค JEG Tellem โ€ข ๐ŸŽผ Nyimbo Ya Chikondi โ€ข โฑ๏ธ 3:07
๐ŸŽต 2287 characters
โฑ๏ธ 3:07 duration
๐Ÿ†” ID: 12961946

๐Ÿ“œ Lyrics

Ase (yeah)
Babe yathu ikuti
Timangoyimba
Za mavuto chani chani
Nde tiyimbe ka nyimbo ka love song wayiziwa eti
Koma osati ija yokuti Ndakudalila
Mhuu Wayiziwa imene ija
Ingokhala inayake ija wayiziwa
Ndizimenya ma Yahman yah
(Kumabwera ma) nkhani yake Yabanja
Chani chani chani chani chani Yapanja
Eheee

Bae (yahman yah)
Ndibwera kwanu azandiziwe (amama)
Wakonda JEG kusiya guy (ya ndlama)
Ili ndi bima,jeep (ndi hammer)
Ine dentist ndine Mfana (wa Khama)
Ndiwe wabho sundipangilA (matama)
Siwe Traore monga ma bebi (ADama)
Ngawu Monada amakonda zo (gadama)

Pa den ndizakuphikra (phwanyanya)
Mipunga mipiru (khwanyanya)
Pa nkhani yokongolayi (unanyanya)
Pokwana unadusa uma (kwanyanya)
Enawa zimawa di (nyanyanya)
Zoti umawa chi (nyanyanya)
Koma ndizawa fi (nyanyanya)
Ndimadana ndizopusa za (nyonyonyo)

Umafilla nyimbo za Chikondi
Nkhani ndabwera nayo rose
Zokutuluka nde ndi Ngozi
Tanena mhhu Eh
Wati umafilla nyimbo za Chikondi - (Yahman yah)
Nkhani ndabwera nayo rose - (njabanja)
Zokutuluka nde ndi Ngozi - (nzapanja)
Tanena mhhu Eh

Akazi enawa akuchepela kababa
Ndaganiza zokutengela kwa baba
Chifukwa mitima yathu wababa
Ifeyo akuchimuna tikudabwa bwa
Sine player Idana olo Gaba
Sine wa ndale Nankhumwa olo Ntaba
Nkhawa zanga wafufuta rubber ber
Iyi ndi love ya Ghetto Kabwababwa

Eko Chikondi iwe cha Phamwamwa
Chikukwana tsiku lonse mpaka utsamwa
Suli ngati akazi otokota Akamwa
Umadana ndi za nkutu zamkamwa
Ndipatse kiss mhuu Mwa mwa mwa
Bwerani boiz muzawaziwe alamu anu
Honey moon izayambila Balaka, kuvaya ku Lusaka
Kukathela Panama

Umafilla nyimbo za Chikondi
Nkhani ndabwera nayo rose
Zokutuluka nde ndi Ngozi
Tanena mhhu Eh
Wati umafilla nyimbo za Chikondi - (Yahman yah)
Nkhani ndabwera nayo rose - (njabanja)
Zokutuluka nde ndi Ngozi - (nzapanja)
Tanena mhhu Eh
Umafilla nyimbo za Chikondi
Nkhani ndabwera nayo rose
Zokutuluka nde ndi Ngozi
Tanena mhhu Eh
Wati umafilla nyimbo za Chikondi - (Yahman yah)
Nkhani ndabwera nayo rose - (njabanja)
Zokutuluka nde ndi Ngozi - (nzapanja)
Tanena mhhu Eh

Aaah mhhu
Nde ma guy
Nkazi wanga video call nde ayi ayi
Muzimupasa moni yekha ndi babayi
Mukationa muzikwapuka walayi
Walayi?
Sinkhazayi
Koma namuvutikilatu mwanayi
Ankachita kumati lero ndikanayi
Wandikwezapo njinga katatu mtsikanayi
Ase Jizzy, si Kanayi?
Mhhu kaya

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:05.82] Ase (yeah)
[00:08.01] Babe yathu ikuti
[00:09.45] Timangoyimba
[00:10.24] Za mavuto chani chani
[00:12.38] Nde tiyimbe ka nyimbo ka love song wayiziwa eti
[00:15.05] Koma osati ija yokuti Ndakudalila
[00:17.59] Mhuu Wayiziwa imene ija
[00:19.92] Ingokhala inayake ija wayiziwa
[00:21.98] Ndizimenya ma Yahman yah
[00:24.13] (Kumabwera ma) nkhani yake Yabanja
[00:25.88] Chani chani chani chani chani Yapanja
[00:27.85] Eheee
[00:28.53] Bae (yahman yah)
[00:30.57] Ndibwera kwanu azandiziwe (amama)
[00:32.87] Wakonda JEG kusiya guy (ya ndlama)
[00:35.06] Ili ndi bima,jeep (ndi hammer)
[00:37.56] Ine dentist ndine Mfana (wa Khama)
[00:39.77] Ndiwe wabho sundipangilA (matama)
[00:42.25] Siwe Traore monga ma bebi (ADama)
[00:44.66] Ngawu Monada amakonda zo (gadama)
[00:47.12] Pa den ndizakuphikra (phwanyanya)
[00:49.79] Mipunga mipiru (khwanyanya)
[00:52.03] Pa nkhani yokongolayi (unanyanya)
[00:54.45] Pokwana unadusa uma (kwanyanya)
[00:56.74] Enawa zimawa di (nyanyanya)
[00:59.28] Zoti umawa chi (nyanyanya)
[01:01.53] Koma ndizawa fi (nyanyanya)
[01:03.82] Ndimadana ndizopusa za (nyonyonyo)
[01:06.04] Umafilla nyimbo za Chikondi
[01:08.60] Nkhani ndabwera nayo rose
[01:10.98] Zokutuluka nde ndi Ngozi
[01:13.48] Tanena mhhu Eh
[01:15.32] Wati umafilla nyimbo za Chikondi - (Yahman yah)
[01:17.93] Nkhani ndabwera nayo rose - (njabanja)
[01:20.12] Zokutuluka nde ndi Ngozi - (nzapanja)
[01:22.61] Tanena mhhu Eh
[01:25.19] Akazi enawa akuchepela kababa
[01:27.61] Ndaganiza zokutengela kwa baba
[01:30.03] Chifukwa mitima yathu wababa
[01:32.47] Ifeyo akuchimuna tikudabwa bwa
[01:34.75] Sine player Idana olo Gaba
[01:37.12] Sine wa ndale Nankhumwa olo Ntaba
[01:39.42] Nkhawa zanga wafufuta rubber ber
[01:41.88] Iyi ndi love ya Ghetto Kabwababwa
[01:44.09] Eko Chikondi iwe cha Phamwamwa
[01:46.60] Chikukwana tsiku lonse mpaka utsamwa
[01:48.93] Suli ngati akazi otokota Akamwa
[01:51.46] Umadana ndi za nkutu zamkamwa
[01:53.86] Ndipatse kiss mhuu Mwa mwa mwa
[01:56.19] Bwerani boiz muzawaziwe alamu anu
[01:58.92] Honey moon izayambila Balaka, kuvaya ku Lusaka
[02:02.18] Kukathela Panama
[02:02.88] Umafilla nyimbo za Chikondi
[02:05.56] Nkhani ndabwera nayo rose
[02:08.03] Zokutuluka nde ndi Ngozi
[02:10.33] Tanena mhhu Eh
[02:12.24] Wati umafilla nyimbo za Chikondi - (Yahman yah)
[02:15.07] Nkhani ndabwera nayo rose - (njabanja)
[02:17.55] Zokutuluka nde ndi Ngozi - (nzapanja)
[02:19.89] Tanena mhhu Eh
[02:21.88] Umafilla nyimbo za Chikondi
[02:24.63] Nkhani ndabwera nayo rose
[02:27.06] Zokutuluka nde ndi Ngozi
[02:29.41] Tanena mhhu Eh
[02:31.27] Wati umafilla nyimbo za Chikondi - (Yahman yah)
[02:33.98] Nkhani ndabwera nayo rose - (njabanja)
[02:36.41] Zokutuluka nde ndi Ngozi - (nzapanja)
[02:38.77] Tanena mhhu Eh
[02:40.11] Aaah mhhu
[02:41.15] Nde ma guy
[02:42.24] Nkazi wanga video call nde ayi ayi
[02:44.45] Muzimupasa moni yekha ndi babayi
[02:46.87] Mukationa muzikwapuka walayi
[02:49.17] Walayi?
[02:50.14] Sinkhazayi
[02:51.67] Koma namuvutikilatu mwanayi
[02:53.97] Ankachita kumati lero ndikanayi
[02:56.28] Wandikwezapo njinga katatu mtsikanayi
[02:58.73] Ase Jizzy, si Kanayi?
[03:01.33] Mhhu kaya
[03:03.18]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings