Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Kuli Kashi

๐Ÿ‘ค Base cube โ€ข ๐ŸŽผ Letting Things Go โ€ข โฑ๏ธ 3:05
๐ŸŽต 1647 characters
โฑ๏ธ 3:05 duration
๐Ÿ†” ID: 12981390

๐Ÿ“œ Lyrics

Back Then Tikuyamba Siznali Chonchi
Timkangofuna ku hita
Pano tinapita ndizopita kuti timangopita
Kufika ngati Water board loza komwe Kuli Mita(metre)
Funa ku limba i've been soft for so long
Thumba mwanga ndikungofuna kulimba

Eeeeh eeeeeh
Eeeh loza kuli Cash ase
Eeeeh eeeeeh
Eeeh loza kuli Cash ase
Eeeeh eeeeeh
Eeeh loza Cash ase

Spe uli cold ngati Ice cube (cold)
BT kulimka ndi base Cube (BTz)
Views kukwera pa Youtube (Youtube)
Ku plugga zozunguza mutu (kush)
Dm kwazaza ti Nkhuku (Chicks)
Utha kusokoneza ndiku Dhudhu(poultry)
Olo utaseka Makutu
Unayamba kundimva Gwamba ali dhuntu(dhunntu)
Back in 018
Ndisanavaye ku Area 18
Before i lost my Queen
Rap isanayambe ku payer Rent
Mmutu mwanga muli Tint
Tisaku Runner mkomwe Business
Ma Goat akupempha ma Remix
I had to Go,i figured it out
My self sungandipusise

Loza kuli Cash ase
Loza kuli Cash ase
Loza Cash ase

Ndalama zimandikonda
Ndikasanja ndimakondwa
Kukhala m'maluzi ndi ukapolo ase I wanna be freed ngati Honda
Chilichonse timabosha
Look we ain't got a chip on our shoulder
But you know that i'm looking so flyer now
Men I don't even need a poster
Yeh you know that we keep it a hundred
Sitidanda tikapeza 50
Timathamangisa zima business
Ngati tamva kubwera a city
Oh yeh they calling me a big dawg
Ambirinu mumanditcha biggy
Ndikupanga zi ndalama zanga zanga
Ndimatchila ndi achina Piksy
Ndimatchila ndi achina Crispy
Pa chi weekend, tikusokoneza
Magaye ambiri amazipopa kah
Ifeyo timangobowoleza
Ifeyo timangobwera kutenga zi cash kutenga zi dolla
Koma ndi mbola
Chifukwa nde tima baller
Eeii
Eeeish eeishh eeh

Loza kuli Cash ase
Loza kuli Cash ase
Loza Cash ase iwee
Malawian

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:29.27] Back Then Tikuyamba Siznali Chonchi
[00:32.15] Timkangofuna ku hita
[00:33.77] Pano tinapita ndizopita kuti timangopita
[00:37.60] Kufika ngati Water board loza komwe Kuli Mita(metre)
[00:41.87] Funa ku limba i've been soft for so long
[00:45.03] Thumba mwanga ndikungofuna kulimba
[00:47.91] Eeeeh eeeeeh
[00:49.58] Eeeh loza kuli Cash ase
[00:51.15] Eeeeh eeeeeh
[00:52.12] Eeeh loza kuli Cash ase
[00:54.20] Eeeeh eeeeeh
[00:56.46] Eeeh loza Cash ase
[01:00.82] Spe uli cold ngati Ice cube (cold)
[01:02.97] BT kulimka ndi base Cube (BTz)
[01:04.81] Views kukwera pa Youtube (Youtube)
[01:06.97] Ku plugga zozunguza mutu (kush)
[01:09.08] Dm kwazaza ti Nkhuku (Chicks)
[01:10.70] Utha kusokoneza ndiku Dhudhu(poultry)
[01:12.47] Olo utaseka Makutu
[01:14.30] Unayamba kundimva Gwamba ali dhuntu(dhunntu)
[01:16.94] Back in 018
[01:18.21] Ndisanavaye ku Area 18
[01:20.31] Before i lost my Queen
[01:21.98] Rap isanayambe ku payer Rent
[01:24.51] Mmutu mwanga muli Tint
[01:26.15] Tisaku Runner mkomwe Business
[01:28.25] Ma Goat akupempha ma Remix
[01:30.05] I had to Go,i figured it out
[01:31.96] My self sungandipusise
[01:35.69] Loza kuli Cash ase
[01:39.02] Loza kuli Cash ase
[01:43.02] Loza Cash ase
[01:45.63] Ndalama zimandikonda
[01:49.39] Ndikasanja ndimakondwa
[01:51.63] Kukhala m'maluzi ndi ukapolo ase I wanna be freed ngati Honda
[01:55.61] Chilichonse timabosha
[01:57.42] Look we ain't got a chip on our shoulder
[01:59.03] But you know that i'm looking so flyer now
[02:01.18] Men I don't even need a poster
[02:03.27] Yeh you know that we keep it a hundred
[02:04.75] Sitidanda tikapeza 50
[02:06.70] Timathamangisa zima business
[02:08.54] Ngati tamva kubwera a city
[02:11.38] Oh yeh they calling me a big dawg
[02:12.47] Ambirinu mumanditcha biggy
[02:14.26] Ndikupanga zi ndalama zanga zanga
[02:16.13] Ndimatchila ndi achina Piksy
[02:18.25] Ndimatchila ndi achina Crispy
[02:20.14] Pa chi weekend, tikusokoneza
[02:22.40] Magaye ambiri amazipopa kah
[02:24.06] Ifeyo timangobowoleza
[02:26.18] Ifeyo timangobwera kutenga zi cash kutenga zi dolla
[02:29.51] Koma ndi mbola
[02:31.48] Chifukwa nde tima baller
[02:33.86] Eeii
[02:34.51] Eeeish eeishh eeh
[02:37.44] Loza kuli Cash ase
[02:40.91] Loza kuli Cash ase
[02:44.88] Loza Cash ase iwee
[02:54.29] Malawian
[02:55.89]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings