Mabala
๐ต 1472 characters
โฑ๏ธ 3:09 duration
๐ ID: 13120939
๐ Lyrics
Oooh
Pena mtima umawawa (mtima umawawa, mtima umawawa)
Achuluka ndi mabala (ndi mabala, mabala)

Achuluka ndi mabala (ndi mabala, ndi mabala) no, ey
Osanama ndikukhala movutika, ngakhale ndimalimbika
Loto mkukhala lopita Jamaica
Poti njira ya Jamaica
Koma ngakhale ndipushe ndilimbikire bwa
Kungochuluka ndi kupondelezedwa
Kukhomeleledwa komanso kuphweketsedwa
Eti olo nkome bwanji singapose thobwa
Amayine, Malawi ndisimba bwanji mtendere mu umphawi
Potitu zonsetu ndi nthawi
Mkumbuka mawu ananena mayi
Pena mtima umawawa (umawawa mtima)
Achuluka ndi mabala (achuluka mabala)
Pena mtima umawawa (umawawa, mtima)
Achuluka ndi mabala (Achuluka luka mabala)
Mabala, mabala, mabala
Mabala, mabala, ey
Mchere wa muthukuta ndi misonzi yanga (mmh)
Ndiye mankhwala amabala anga (anga)
Ambiri simusamala za mavuto anga (mmh)
Jehovah yekha ndiye ngaka yanga (yanga yeah)
Kuchokera pobadwa, n'nadziwa kulira nsanadziwe kuseka
M'mene ndimkakula, n'nadziwa magobo nsanadziwe kusewela
Mtima umawawa, umawawa mtima
Achuluka ndi mabala, achuluka ndi mabala
Pena mtima umawawa, umawawa mtima
Achuluka ndi mabala, achulula luka mabala
Ndukukuwuzani misozi yanga itha kukumizani
Litha kukukulani thukuta lomwe ndakhetsa mu mtima
Umawawa, umawawa mtima

Umawawa mtima
Achulula mabala
Umawawa mtima
Achuluka luka mabala

โฑ๏ธ Synced Lyrics
[00:04.57] Oooh
[00:08.76] Pena mtima umawawa (mtima umawawa, mtima umawawa)
[00:14.77] Achuluka ndi mabala (ndi mabala, mabala)
[00:19.67] Pena mtima umawawa (mtima umawawa, mtima umawawa)
[00:24.93] Achuluka ndi mabala (ndi mabala, ndi mabala) no, ey
[00:29.90] Osanama ndikukhala movutika, ngakhale ndimalimbika
[00:35.04] Loto mkukhala lopita Jamaica
[00:37.40] Poti njira ya Jamaica
[00:39.22] Koma ngakhale ndipushe ndilimbikire bwa
[00:42.33] Kungochuluka ndi kupondelezedwa
[00:44.84] Kukhomeleledwa komanso kuphweketsedwa
[00:46.94] Eti olo nkome bwanji singapose thobwa
[00:49.71] Amayine, Malawi ndisimba bwanji mtendere mu umphawi
[00:54.96] Potitu zonsetu ndi nthawi
[00:56.98] Mkumbuka mawu ananena mayi
[00:59.76] Pena mtima umawawa (umawawa mtima)
[01:04.39] Achuluka ndi mabala (achuluka mabala)
[01:09.57] Pena mtima umawawa (umawawa, mtima)
[01:14.65] Achuluka ndi mabala (Achuluka luka mabala)
[01:21.48] Mabala, mabala, mabala
[01:26.74] Mabala, mabala, ey
[01:29.92] Mchere wa muthukuta ndi misonzi yanga (mmh)
[01:33.02] Ndiye mankhwala amabala anga (anga)
[01:35.08] Ambiri simusamala za mavuto anga (mmh)
[01:37.67] Jehovah yekha ndiye ngaka yanga (yanga yeah)
[01:41.84] Kuchokera pobadwa, n'nadziwa kulira nsanadziwe kuseka
[01:46.96] M'mene ndimkakula, n'nadziwa magobo nsanadziwe kusewela
[01:50.25] Mtima umawawa, umawawa mtima
[01:54.84] Achuluka ndi mabala, achuluka ndi mabala
[02:00.10] Pena mtima umawawa, umawawa mtima
[02:05.06] Achuluka ndi mabala, achulula luka mabala
[02:12.71] Ndukukuwuzani misozi yanga itha kukumizani
[02:16.98] Litha kukukulani thukuta lomwe ndakhetsa mu mtima
[02:20.73] Umawawa, umawawa mtima
[02:24.78] Achuluka ndi mabala, achuluka ndi mabala
[02:30.31] Pena mtima umawawa, umawawa mtima
[02:34.94] Achuluka ndi mabala, achulula luka mabala
[02:42.13] Umawawa mtima
[02:47.21] Achulula mabala
[02:52.36] Umawawa mtima
[02:57.26] Achuluka luka mabala
[03:03.25]