Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Time

๐Ÿ‘ค Praise Umali โ€ข ๐ŸŽผ Time โ€ข โฑ๏ธ 3:36
๐ŸŽต 1248 characters
โฑ๏ธ 3:36 duration
๐Ÿ†” ID: 13320363

๐Ÿ“œ Lyrics

Anzanga akumati ndizitolera
Ati "I need time"
I need time
I need time
I'm just Tryna take it easy, easy
Koma mtima umawawabe sometimes, believe me

Koma ati zonse zimatha, ma feeling amatha
Ingodekha zimatha, dekha zimatha
Usalire zimatha, ululu umatha
Ingodekha zimatha
Chikhala nthawi ndi mankhwala, nkana chila dzana
Mwina lakula ndi balali, mtima umawawa
Ngati nthawi ndi mankhwala, bwezi ntachila dzana
Kapena mwina mawali

Komabe mwina I just need time
I need time
Ndichila I just need time
I need time

Mwina ndiyese therapy
'Cause it's been a while now since I felt like me
Olo ndingodikila (Ndingodikila), zikhala better (Zikhala better)
Usazitengera iwe, ndizamdziko izi

Nde ati zonse zimatha, ma feeling amatha
Ingodekha zimatha, dekha zimatha
Usalire zimatha, ululu umatha
Ingodekha zimatha
Koma chikhala nthawi ndi mankhwala, nkana chila dzana
Mwina lakula ndi balali, mtima umawawa
Ngati nthawi ndi mankhwala, bwezi nditachila dzana
Kapena mwina mawali

Mwina I just need time (Maybe I need sometime, I need sometime)
I need time (I need sometime, maybe I need sometime)
Ndichila I just need time (I need sometime, I need sometime)
I need time (I need sometime, maybe I need sometime)

I need time
I need time
I need time
I need time

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings