Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Kwanu Ndi Kwanu

๐Ÿ‘ค JEG Tellem โ€ข ๐ŸŽผ Me VS mE โ€ข โฑ๏ธ 4:07
๐ŸŽต 2216 characters
โฑ๏ธ 4:07 duration
๐Ÿ†” ID: 14091309

๐Ÿ“œ Lyrics

Woyee yeah yeah
Osamayiwala kwanu
Osamayiwala

Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mhuuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Nthengo mudalaka njoka aaah

Penapake zikavuta iwe
Ndikwanube
Usamachite manyazi
Ndikwanube
Utha kubwerera konko
Ndikwanube ah ah aaaaah

Osayi wala
Dzuwa likawala
Yemwe anakubala
Yemwe anakusamala
Pamene ukudwala
Usanakwela ladder
Kwanu kwanu nthengo mudalaka njoka
Uzakufunabe olo utachoka
Mukanyozela muzatenga matsoka
Osalora azako aziku locker

Kwanu Ndi Kwanu mmhu
Nthengo mudalaka njoka aah
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah

Munachoka kunyumba kalekale mwati munatola Ka joker
Koma muzabwerabe kwanu nthengo munalaka Ka njoka
Mwasintha mawanga mwasintha khungu mapeto Ake ndi matsoka
Muzatipeza zinthu zikazavuta Pano tingopenya ndi maso
Pa maliro simumapezeka
Kumanda simumapezeka
Koma kuti mugone pansi lero lomwe kumanda omwewo mupezeka
Anapita kalekale kokawonekela eh
Koma kaphiri kakwawo sikaonekela eh
Pena nkumati njokayo mwina nthengo yasochela
Koma azatipezabe mizimu sikukondwera

Kwanu Ndi Kwanu mmhu
Nthengo mudalaka njoka aah
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah

Yeah
Galu amanyada pakwawo nanga iweyo ulekelanji
Uzigomela Malawi kwanu kuno sungasowe mtaji
Funsa neba amasililanji
Mtendere umayambila chitipa kuthela Ku nsanje
Warm heart Ku mpanje
Uzingotakata mpakana uzatsegula maloko
Kutukula Dela lakwanu akhale ako maloto
Kwanu usakuluzile hope
Ukavaya abroad kusaka guap
Tsiku lomwe uzafike pa top
Kwanu uzakuyikeso pa map
Mukanabwera
Mwakhalitsa
Anzanu ochenjela
Goshen amangitsa
Lemme explain
Kulibeko Malo ngati pa den
Tufunika mindset change
Osangokhalila kupanga complain
Yeah yeah

Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mhuuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Nthengo mudalaka njoka aaah

Kamdothi iwe bwerera Ku nyumba iwe
Kamdothi iwe uthela moyenda iwe
Kamdothi iwe aaaaaah
Kamdothi iwe aaaaaah
Kwanu Ndi Kwanu mfana
Town ikasolobana
Ukumbuke padzana
Bwerera Kwa Amama

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:04.79] Woyee yeah yeah
[00:08.77] Osamayiwala kwanu
[00:12.40] Osamayiwala
[00:13.73] Kwanu Ndi Kwanu mhuu
[00:17.01] Nthengo mudalaka njoka aaah
[00:20.81] Kwanu Ndi Kwanu mhuuu
[00:24.48] Nthengo mudalaka njoka aaah
[00:27.80] Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
[00:29.95] Ndi kwanube
[00:31.05] Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh
[00:33.35] Ndi kwanube
[00:34.75] Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
[00:36.68] Ndi kwanube
[00:38.12] Nthengo mudalaka njoka aaah
[00:41.32] Penapake zikavuta iwe
[00:43.63] Ndikwanube
[00:45.08] Usamachite manyazi
[00:46.93] Ndikwanube
[00:48.40] Utha kubwerera konko
[00:50.52] Ndikwanube ah ah aaaaah
[00:54.93] Osayi wala
[00:56.98] Dzuwa likawala
[00:58.67] Yemwe anakubala
[01:00.35] Yemwe anakusamala
[01:02.09] Pamene ukudwala
[01:03.53] Usanakwela ladder
[01:08.77] Kwanu kwanu nthengo mudalaka njoka
[01:11.87] Uzakufunabe olo utachoka
[01:14.95] Mukanyozela muzatenga matsoka
[01:18.93] Osalora azako aziku locker
[01:22.45] Kwanu Ndi Kwanu mmhu
[01:25.94] Nthengo mudalaka njoka aah
[01:29.40] Kwanu Ndi Kwanu mhuu
[01:32.86] Nthengo mudalaka njoka aaah
[01:36.07] Munachoka kunyumba kalekale mwati munatola Ka joker
[01:39.51] Koma muzabwerabe kwanu nthengo munalaka Ka njoka
[01:43.18] Mwasintha mawanga mwasintha khungu mapeto Ake ndi matsoka
[01:46.25] Muzatipeza zinthu zikazavuta Pano tingopenya ndi maso
[01:49.91] Pa maliro simumapezeka
[01:51.43] Kumanda simumapezeka
[01:53.11] Koma kuti mugone pansi lero lomwe kumanda omwewo mupezeka
[01:56.47] Anapita kalekale kokawonekela eh
[01:59.89] Koma kaphiri kakwawo sikaonekela eh
[02:03.09] Pena nkumati njokayo mwina nthengo yasochela
[02:06.89] Koma azatipezabe mizimu sikukondwera
[02:09.82] Kwanu Ndi Kwanu mmhu
[02:13.53] Nthengo mudalaka njoka aah
[02:17.08] Kwanu Ndi Kwanu mhuu
[02:20.65] Nthengo mudalaka njoka aaah
[02:23.34] Yeah
[02:24.40] Galu amanyada pakwawo nanga iweyo ulekelanji
[02:27.49] Uzigomela Malawi kwanu kuno sungasowe mtaji
[02:30.62] Funsa neba amasililanji
[02:33.28] Mtendere umayambila chitipa kuthela Ku nsanje
[02:35.95] Warm heart Ku mpanje
[02:38.02] Uzingotakata mpakana uzatsegula maloko
[02:41.61] Kutukula Dela lakwanu akhale ako maloto
[02:44.82] Kwanu usakuluzile hope
[02:45.89] Ukavaya abroad kusaka guap
[02:47.57] Tsiku lomwe uzafike pa top
[02:49.55] Kwanu uzakuyikeso pa map
[02:51.94] Mukanabwera
[02:53.71] Mwakhalitsa
[02:55.45] Anzanu ochenjela
[02:56.60] Goshen amangitsa
[02:58.48] Lemme explain
[02:59.66] Kulibeko Malo ngati pa den
[03:01.68] Tufunika mindset change
[03:02.64] Osangokhalila kupanga complain
[03:04.48] Yeah yeah
[03:05.52] Kwanu Ndi Kwanu mhuu
[03:08.45] Nthengo mudalaka njoka aaah
[03:11.66] Kwanu Ndi Kwanu mhuuu
[03:15.01] Nthengo mudalaka njoka aaah
[03:18.75] Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
[03:21.35] Ndi kwanube
[03:22.43] Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh
[03:24.68] Ndi kwanube
[03:25.84] Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
[03:27.89] Ndi kwanube
[03:29.42] Nthengo mudalaka njoka aaah
[03:34.44] Kamdothi iwe bwerera Ku nyumba iwe
[03:37.98] Kamdothi iwe uthela moyenda iwe
[03:41.25] Kamdothi iwe aaaaaah
[03:44.63] Kamdothi iwe aaaaaah
[03:47.93] Kwanu Ndi Kwanu mfana
[03:49.78] Town ikasolobana
[03:51.75] Ukumbuke padzana
[03:53.35] Bwerera Kwa Amama
[03:58.47]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings