Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

My Daily Worship

๐Ÿ‘ค Gwamba โ€ข ๐ŸŽผ True Independence โ€ข โฑ๏ธ 3:48
๐ŸŽต 1851 characters
โฑ๏ธ 3:48 duration
๐Ÿ†” ID: 14172168

๐Ÿ“œ Lyrics

I have never seen, no one like you (no one like you)
No one like you (no one like you)
Yesu (Yesu)

I have never seen, no one like you (no one like you)
No one like you (no one like you)
Yesu (Yesu)

Ambuye (Ambuye)
Ambuye (Ambuye)
Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye)
Ambuye (Ambuye)

Ambuye (Ambuye), Ndikuthokoza Ambuye
Eeh eh eh

Iyi ndi nyimbo yafuko langa, my daily worship
Ndikuvutika simunandisiye chonchi
Kundionesa ufumu wanu kundipasa chi plot
Nde kulikose ndingapiteko tili limodzi

Abale ndi alongo zikavuta amathawa
Mavuto, pa mtendele simumansintha ma colour
Nde zingavute bwanji ndimayesesa ndisadande
Poti masiku sakoma onse, ndi nthawi chabe

Iyi ndi daily worship, nyimbo yafuko langa
Kenako ukamvera uzipezamo ka bata
Osamathamangila kunena kuti sanayankhe

Chifukwa olo mpweya tikupumau ndi wake
Pali chinthu chimodzi chomwe mumalakwisa brazi

Mufuna mudwale kaye kuti muyamikire nthanzi
Wina amwalire kuti muyamikire moyo
Akachedwa kuyankha mumasiya kukhala loyal

Ndeno Tate wanga ndufuna kukhala munthu wa humble
Poti ndikuziwa mumapasa, mumalanda

Komanso ndukufuna ndikhale chitsanzo
Mfana wa mature poti chibwana chimalanda

Kuchepesa anga, bible likhale mzanga
Munthu kundiyamba ine kukhululuka nsanga

Kupewa ma blanda, Jajah mu mtima mwanga
Tsiku lomalidza kuchongetsa dzina langa

Ambuye (yea yea yea yea)
Ambuye (yea yea yea yea)
Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye)

Ambuye (yea yea yea yea)
Ambuye (yea yea yea yea)
Ndikuthokoza Ambuye (Ambuye eeh)
Uuh uh uuh

I have never seen, no one like you (no one like you)
No one like you (no one like you)
Yesu (Yesu)

I have never seen, no one like you (no one like you)
No one like you (no one like you)
Yesu (Yesu)

Ambuye
Ambuye (no one like you)
Ndikuthokoza Ambuye (Yesu)

Ambuye
Ambuye (no one like you)
Ndikuthokoza Ambuye (Yesu)
Uuh yeah yeah
Uuh yeah yeah

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:22.27] I have never seen, no one like you (no one like you)
[00:28.08] No one like you (no one like you)
[00:29.91] Yesu (Yesu)
[00:34.07] I have never seen, no one like you (no one like you)
[00:39.10] No one like you (no one like you)
[00:42.25] Yesu (Yesu)
[00:45.44] Ambuye (Ambuye)
[00:48.65] Ambuye (Ambuye)
[00:53.27] Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye)
[00:57.27] Ambuye (Ambuye)
[01:00.24] Ambuye (Ambuye), Ndikuthokoza Ambuye
[01:07.67] Eeh eh eh
[01:08.87] Iyi ndi nyimbo yafuko langa, my daily worship
[01:11.88] Ndikuvutika simunandisiye chonchi
[01:14.73] Kundionesa ufumu wanu kundipasa chi plot
[01:18.03] Nde kulikose ndingapiteko tili limodzi
[01:21.08] Abale ndi alongo zikavuta amathawa
[01:23.36] Mavuto, pa mtendele simumansintha ma colour
[01:26.62] Nde zingavute bwanji ndimayesesa ndisadande
[01:29.37] Poti masiku sakoma onse, ndi nthawi chabe
[01:33.02] Iyi ndi daily worship, nyimbo yafuko langa
[01:35.96] Kenako ukamvera uzipezamo ka bata
[01:38.20] Osamathamangila kunena kuti sanayankhe
[01:40.87] Chifukwa olo mpweya tikupumau ndi wake
[01:44.03] Pali chinthu chimodzi chomwe mumalakwisa brazi
[01:47.36] Mufuna mudwale kaye kuti muyamikire nthanzi
[01:50.36] Wina amwalire kuti muyamikire moyo
[01:53.41] Akachedwa kuyankha mumasiya kukhala loyal
[01:55.89] Ndeno Tate wanga ndufuna kukhala munthu wa humble
[01:59.23] Poti ndikuziwa mumapasa, mumalanda
[02:02.82] Komanso ndukufuna ndikhale chitsanzo
[02:05.47] Mfana wa mature poti chibwana chimalanda
[02:08.12] Kuchepesa anga, bible likhale mzanga
[02:11.33] Munthu kundiyamba ine kukhululuka nsanga
[02:14.04] Kupewa ma blanda, Jajah mu mtima mwanga
[02:16.93] Tsiku lomalidza kuchongetsa dzina langa
[02:19.89] Ambuye (yea yea yea yea)
[02:22.50] Ambuye (yea yea yea yea)
[02:26.99] Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye)
[02:30.67] Ambuye (yea yea yea yea)
[02:33.66] Ambuye (yea yea yea yea)
[02:38.53] Ndikuthokoza Ambuye (Ambuye eeh)
[02:41.44] Uuh uh uuh
[02:43.54] I have never seen, no one like you (no one like you)
[02:47.82] No one like you (no one like you)
[02:50.87] Yesu (Yesu)
[02:54.88] I have never seen, no one like you (no one like you)
[02:57.70] No one like you (no one like you)
[03:03.74] Yesu (Yesu)
[03:06.00] Ambuye
[03:09.67] Ambuye (no one like you)
[03:13.66] Ndikuthokoza Ambuye (Yesu)
[03:17.97] Ambuye
[03:20.97] Ambuye (no one like you)
[03:25.63] Ndikuthokoza Ambuye (Yesu)
[03:29.70] Uuh yeah yeah
[03:31.73] Uuh yeah yeah
[03:47.60]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings