Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Get There

๐Ÿ‘ค Gwamba โ€ข ๐ŸŽผ Get There โ€ข โฑ๏ธ 3:51
๐ŸŽต 1911 characters
โฑ๏ธ 3:51 duration
๐Ÿ†” ID: 14172278

๐Ÿ“œ Lyrics

Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there

Yeah, aish
Pena ngati mwina ndingogivah
Ndikupemphera koma mbuye sakundimva
Njala, nthenda, mavuto andiliza
Ndikuwona ngati mwina bible limatinamiza
Zitseko zamadalitso ndayesa ku knocker
Mbuye sakutsegula padakali poloka
Ndikulakwitsa pati? Mwina ndikakwere phiri
Ndiwuzeni zochita, mavutowa ndi ambiri

Mafunso achuluka koma palibe oyankha
Nde m'malo molira timadzukabe nkukankha
Mtima ukuwawa ife timasekelera
Timadziwa tsiku lina madalitso adzatigwera, yes

Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there

Aish, anakupatsa mimba nkuyikana
Usowa chochita poti udakali mwana
Kukanika kugona, usiku kumangolira
Dekha, ambuye Yesu adzakupatsa njira
Unalemba mayenso osakhonza? Lembanso
Kumenya hustle osatheka, menyanso
Osagivah iwe simfana wa weak
Ngati pano sizutheka yesa kumenyanso repeat

Kuli mavuto odetsa nkhawa
Usalire yang'ana za mawa

Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there

Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there

You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:21.44] Everytime you're feeling down
[00:23.61] Everytime you're feeling weak
[00:25.95] Yang'ana kumwamba you'll get there
[00:30.98] Everytime you're feeling down
[00:33.23] Everytime you're feeling weak
[00:36.16] Yang'ana kumwamba you'll get there
[00:41.15] You'll get there, you'll get there
[00:45.89] Yang'ana kumwamba you'll get there
[00:48.02] Yeah, aish
[00:49.76] Pena ngati mwina ndingogivah
[00:51.77] Ndikupemphera koma mbuye sakundimva
[00:54.15] Njala, nthenda, mavuto andiliza
[00:56.36] Ndikuwona ngati mwina bible limatinamiza
[00:58.80] Zitseko zamadalitso ndayesa ku knocker
[01:01.17] Mbuye sakutsegula padakali poloka
[01:03.63] Ndikulakwitsa pati? Mwina ndikakwere phiri
[01:06.00] Ndiwuzeni zochita, mavutowa ndi ambiri
[01:09.07] Mafunso achuluka koma palibe oyankha
[01:11.55] Nde m'malo molira timadzukabe nkukankha
[01:14.02] Mtima ukuwawa ife timasekelera
[01:16.50] Timadziwa tsiku lina madalitso adzatigwera, yes
[01:19.05] Everytime you're feeling down
[01:21.61] Everytime you're feeling weak
[01:25.37] Yang'ana kumwamba you'll get there
[01:29.91] Everytime you're feeling down
[01:32.46] Everytime you're feeling weak
[01:35.38] Yang'ana kumwamba you'll get there
[01:40.19] You'll get there, you'll get there
[01:45.37] Yang'ana kumwamba you'll get there
[01:48.50] Aish, anakupatsa mimba nkuyikana
[01:51.13] Usowa chochita poti udakali mwana
[01:53.21] Kukanika kugona, usiku kumangolira
[01:55.81] Dekha, ambuye Yesu adzakupatsa njira
[01:58.18] Unalemba mayenso osakhonza? Lembanso
[02:00.70] Kumenya hustle osatheka, menyanso
[02:02.65] Osagivah iwe simfana wa weak
[02:05.95] Ngati pano sizutheka yesa kumenyanso repeat
[02:08.35] Kuli mavuto odetsa nkhawa
[02:11.75] Usalire yang'ana za mawa
[02:18.28] Everytime you're feeling down
[02:21.63] Everytime you're feeling weak
[02:24.72] Yang'ana kumwamba you'll get there
[02:29.13] Everytime you're feeling down
[02:31.68] Everytime you're feeling weak
[02:34.73] Yang'ana kumwamba you'll get there
[02:39.30] You'll get there, you'll get there
[02:44.02] Yang'ana kumwamba you'll get there
[02:49.33] Everytime you're feeling down
[02:51.48] Everytime you're feeling weak
[02:54.17] Yang'ana kumwamba you'll get there
[02:58.75] Everytime you're feeling down
[03:01.19] Everytime you're feeling weak
[03:04.43] Yang'ana kumwamba you'll get there
[03:09.37] You'll get there, you'll get there
[03:14.56] Yang'ana kumwamba you'll get there
[03:19.65] You'll get there, you'll get there
[03:24.33] Yang'ana kumwamba you'll get there
[03:27.95]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings