Ngati Inu
๐ต 1929 characters
โฑ๏ธ 3:20 duration
๐ ID: 14172409
๐ Lyrics
Yo
Ndika khala ndekha ndekha
Ndazimitsa phone
Ndangoshala penapake ndili lonely
M'mutu mwangamu mumayenda zambiri
Reflection yeni yeni yomwe ine ndili
Koma ndikakhala fanzi ikuona
Ndimafuna ndidzinama ngati obona
Komano kweni kweni m'manamiza ndani?
Beef thupi ndi nzimu wanga udane
Ndikakhala mu church ndimamenya malilime
Komano nzimu oyera sumakhkala uli ndi ine
Pakamwa pakuthoka koma m'mutu muli zina
Wolungama pamaso koma mkatimu ndi sinner
Ngakhale mchipinda
Mopanda amene akuona
Ulengeni mtima wangawu yeah
Ukhale ngati inu! ooh!
In everything i do! ooh!
Nkhale ngati inu! ooh!, (mfanane nanu Baba)
In everything i do! ooh!, (mfanane nanu Baba)
Nde in everything i do
Mundithandize kukhala wodekha
Poti ndinabadwa ndipo ndidzapita ndekha
And it's true ndi zapadzikozi ndimakopeka
Tsoka mukafuna kunditenga osakonzeka
Pena ndimaseka mumtima muli misozi
Anthu amangowona mkamasekelera chonchi
Koma za mu mtima mwanga amadziwa ndi m'modzi
Nde pakati pa dziko ndi Yesu ndisankhe m'modzi

Nkhale ngati inu! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)
In everything i do! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)
Pakamwa panga mupakonze
Mtima wangawu muwupinde
Nzeru zangazi muzipinde
Zochita zanaga ziyamike inu
Munandilenga bwinobwino
Kufuntha kwanga kwawonjeza
Ndizipemphelera chakudya
Olo anzanga asakuwona
Munandilenga kwa ndekha
Munandipatsa za ndekha
Ooh! ooh! ooh!
Ngakhale mchipinda, (ooh!)
Mopanda amene akuona, (alone)

โฑ๏ธ Synced Lyrics
[00:08.12] Yo
[00:09.72] Ndika khala ndekha ndekha
[00:11.28] Ndazimitsa phone
[00:12.79] Ndangoshala penapake ndili lonely
[00:15.00] M'mutu mwangamu mumayenda zambiri
[00:17.63] Reflection yeni yeni yomwe ine ndili
[00:20.26] Koma ndikakhala fanzi ikuona
[00:22.76] Ndimafuna ndidzinama ngati obona
[00:25.19] Komano kweni kweni m'manamiza ndani?
[00:27.42] Beef thupi ndi nzimu wanga udane
[00:30.18] Ndikakhala mu church ndimamenya malilime
[00:32.58] Komano nzimu oyera sumakhkala uli ndi ine
[00:35.26] Pakamwa pakuthoka koma m'mutu muli zina
[00:37.53] Wolungama pamaso koma mkatimu ndi sinner
[00:40.54] Ngakhale mchipinda
[00:42.34] Mopanda amene akuona
[00:45.77] Ulengeni mtima wangawu yeah
[00:48.95] Ukhale ngati inu! ooh!
[00:53.99] In everything i do! ooh!
[00:58.88] Nkhale ngati inu! ooh!, (mfanane nanu Baba)
[01:03.83] In everything i do! ooh!, (mfanane nanu Baba)
[01:10.06] Nde in everything i do
[01:11.20] Mundithandize kukhala wodekha
[01:13.37] Poti ndinabadwa ndipo ndidzapita ndekha
[01:15.89] And it's true ndi zapadzikozi ndimakopeka
[01:18.31] Tsoka mukafuna kunditenga osakonzeka
[01:20.98] Pena ndimaseka mumtima muli misozi
[01:23.30] Anthu amangowona mkamasekelera chonchi
[01:25.75] Koma za mu mtima mwanga amadziwa ndi m'modzi
[01:28.14] Nde pakati pa dziko ndi Yesu ndisankhe m'modzi
[01:30.45] Pena ndimaseka mumtima muli misozi
[01:33.17] Anthu amangowona mkamasekelera chonchi
[01:35.57] Koma za mu mtima mwanga amadziwa ndi m'modzi
[01:38.24] Nde pakati pa dziko ndi Yesu ndisankhe m'modzi
[01:41.27] Ngakhale mchipinda
[01:43.57] Mopanda amene akuona
[01:46.48] Ulengeni mtima wangawu yeah
[01:49.83] Ukhale ngati inu! ooh!
[01:54.63] In everything i do! ooh!
[01:59.78] Nkhale ngati inu! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)
[02:04.76] In everything i do! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)
[02:11.62] Pakamwa panga mupakonze
[02:14.67] Mtima wangawu muwupinde
[02:17.22] Nzeru zangazi muzipinde
[02:19.46] Zochita zanaga ziyamike inu
[02:22.70] Munandilenga bwinobwino
[02:24.97] Kufuntha kwanga kwawonjeza
[02:27.53] Ndizipemphelera chakudya
[02:29.67] Olo anzanga asakuwona
[02:32.36] Munandilenga kwa ndekha
[02:34.61] Munandipatsa za ndekha
[02:37.79] Ooh! ooh! ooh!
[02:41.84] Ngakhale mchipinda, (ooh!)
[02:43.92] Mopanda amene akuona, (alone)
[02:47.07] Ulengeni mtima wangawu yeah
[02:50.12] Ukhale ngati inu! ooh!
[02:55.43] In everything i do! ooh!
[03:00.34] Nkhale ngati inu! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)
[03:05.63] In everything i do! ooh!, (mfanane nanu Baba, mfanane nanu Baba)
[03:19.09]