Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Mamuna Amene Ndili

๐Ÿ‘ค Kelvin Sings โ€ข ๐ŸŽผ Mamuna Amene Ndili โ€ข โฑ๏ธ 3:34
๐ŸŽต 1722 characters
โฑ๏ธ 3:34 duration
๐Ÿ†” ID: 14586385

๐Ÿ“œ Lyrics

Unandipeza ndili lova
Ndilibe kalikonse
Mmatumba mwanga mobooka
Nyumba yopanda khonde
Ndekuti dzuwa likaomba
Mkati khuma kumaonda
Iweyo utandiona
Sindimvetsa chomwe unakonda
Utabwela unandilimbikitsa
Unati ndisabwelele m'mbuyo
Chomwe chinali chako naneso ndi changa
Kuti ndisamasowe tulo

You must be a saint or something
How could you give it all
And ask for nothing in return
Ndikusowa chonena ine
Malangizo ako
Andifikitsa pena ine
Poti ndiine wako
Bwela umunyadile mamuna amene ndili
Kamba ka iwe
Bwela umunyadile mamuna amene ndili
Kamba ka iwe

For I was never enough
I had room for you in my life
Ndizizwa ndichisankho chako ooh
Chokhala nane ngakhale mnyumba mwanga
Mpando munalibe
Pomwe sizinkandiyendela
Unagwada ndikupemphela
Pamene mwayi unatetela
Unandiuza ndimukumbuke namalenga
Ndikamabwela ku ulenje
Mmalo mwa nyama ndi denje
Nkumandilandilabe ndi chimwemwe
Ine pakamwa kakasi
You know pena ndikati ndidye frus
Most of my days I am under the weather
But I believe God gave you to me
To help me keep it together

You must be a saint or something
How could you give it all
And ask for nothing in return
Ndikusowa chonena ine
Malangizo ako
Andifikisa pena ine
Poti ndine wako
Bwela umunyandile mamuna amene ndili
Kamba ka iwee
Chikondi ndachimvesesa
Bwela umunyandile mamuna amene ndili
Kamba ka iwee
Nkhawa zonse unathesa
Bwela umunyandile mamuna amene ndili
Kamba ka iwee
Chikondi ndachimvesesa
Bwela umunyandile mamuna amene ndili
Kamba ka iwee
I'm a better man
Sindikanakwanitsa ndekha
I needed you to get me to where I am right now

Ndikusowa chonena ine
Malangizo ako
Andifikisa pena ine
Poti ndine wako
Bwela umunyandile mamuna amene ndili
Kamba ka iwe
Bwela umunyandile mamuna amene ndili
Kamba ka iwe

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:10.00] Unandipeza ndili lova
[00:13.16] Ndilibe kalikonse
[00:15.31] Mmatumba mwanga mobooka
[00:18.47] Nyumba yopanda khonde
[00:20.63] Ndekuti dzuwa likaomba
[00:23.48] Mkati khuma kumaonda
[00:26.11] Iweyo utandiona
[00:29.04] Sindimvetsa chomwe unakonda
[00:32.12] Utabwela unandilimbikitsa
[00:34.61] Unati ndisabwelele m'mbuyo
[00:37.26] Chomwe chinali chako naneso ndi changa
[00:39.86] Kuti ndisamasowe tulo
[00:42.55] You must be a saint or something
[00:45.81] How could you give it all
[00:49.37] And ask for nothing in return
[00:53.32] Ndikusowa chonena ine
[00:56.79] Malangizo ako
[00:59.23] Andifikitsa pena ine
[01:02.32] Poti ndiine wako
[01:04.37] Bwela umunyadile mamuna amene ndili
[01:07.09] Kamba ka iwe
[01:09.60] Bwela umunyadile mamuna amene ndili
[01:12.51] Kamba ka iwe
[01:15.46]
[01:27.02] For I was never enough
[01:29.62] I had room for you in my life
[01:32.00] Ndizizwa ndichisankho chako ooh
[01:34.79] Chokhala nane ngakhale mnyumba mwanga
[01:36.26] Mpando munalibe
[01:37.56] Pomwe sizinkandiyendela
[01:39.64] Unagwada ndikupemphela
[01:42.21] Pamene mwayi unatetela
[01:44.67] Unandiuza ndimukumbuke namalenga
[01:48.41] Ndikamabwela ku ulenje
[01:50.62] Mmalo mwa nyama ndi denje
[01:53.24] Nkumandilandilabe ndi chimwemwe
[01:55.84] Ine pakamwa kakasi
[01:59.01] You know pena ndikati ndidye frus
[02:02.15] Most of my days I am under the weather
[02:04.88] But I believe God gave you to me
[02:07.23] To help me keep it together
[02:09.96] You must be a saint or something
[02:15.05] How could you give it all
[02:16.50] And ask for nothing in return
[02:20.62] Ndikusowa chonena ine
[02:24.16] Malangizo ako
[02:26.77] Andifikisa pena ine
[02:29.35] Poti ndine wako
[02:31.96] Bwela umunyandile mamuna amene ndili
[02:32.60] Kamba ka iwee
[02:33.77] Chikondi ndachimvesesa
[02:34.43] Bwela umunyandile mamuna amene ndili
[02:38.00] Kamba ka iwee
[02:40.68] Nkhawa zonse unathesa
[02:41.16] Bwela umunyandile mamuna amene ndili
[02:44.82] Kamba ka iwee
[02:47.10] Chikondi ndachimvesesa
[02:48.05] Bwela umunyandile mamuna amene ndili
[02:50.21] Kamba ka iwee
[02:53.47] I'm a better man
[02:55.91] Sindikanakwanitsa ndekha
[02:58.48]
[03:07.16] I needed you to get me to where I am right now
[03:07.68] Ndikusowa chonena ine
[03:08.89] Malangizo ako
[03:09.77] Andifikisa pena ine
[03:13.00] Poti ndine wako
[03:15.23] Bwela umunyandile mamuna amene ndili
[03:18.21] Kamba ka iwe
[03:20.61] Bwela umunyandile mamuna amene ndili
[03:23.48] Kamba ka iwe
[03:24.60]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings