Lipenga
๐ต 2062 characters
โฑ๏ธ 3:33 duration
๐ ID: 14997691
๐ Lyrics
Tsiku lobwera yesu
Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
Tsiku lobwera yesu
Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
Lapilatuu
Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
Nyengo yovuta koma osakhulupilira
Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
Koma jah jah sazakukhulupilira
Akufa adzauka, Kaya osauka
Kaya wachithumba Kaya unali otchuka
Tidzaona misonzi
Panzerepo limodzi
Yeah adzati
Mfana ndakupatsa Zima chance
Lero nde palibe zama story
Mulungu nde salandira Benz
Palibe zoti kuseri ukamukhole
Kaya uli ndi ma doller or rands
Tsiku lomaliza lokha iwe sorry
Palibe zoti Kaya unali ndima fans
Panzere udzakhalapo wekha usaitole
Nde bwanj umachimwabe mulungu ndiwabwno koma osamuyesa
Ngati ufuna kululumuka ukaona tchimo kumaziletsa
Kuyesa angel Michael akuti "no"
Kuyesera king Davide akut "no way"
Ngat uli ochimwa palibe njira ina
Tsiku lomaliza kumwambako usakalowe
Haah

Iwe
Amakupatsa chilichonse chomwe umafuna
Nanga bwanj ulemu osampatsa
Ndizija amakulanda chilichonse, akaona akakupatsa iwe umatasa
Ndeno ma man mutha kulapa kuyisintha nkhani
Satana mdani, ukapusa akuika pa mpani
Azaliza lipenga
Tsiku lomwe lokha mphwanga palibe kuzemba
Azaliza lipenga
Alibe nazo ntchito zoti iwe umafalitsa uthenga
Kaya iwe uma trender
Kaya doctor umachiritsa matenda
Kaya fans ikakuona imapanga
Tsiku lomaliza ndila namalenga

โฑ๏ธ Synced Lyrics
[00:08.03] Tsiku lobwera yesu
[00:11.29] Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
[00:17.07] Tsiku lobwera yesu
[00:20.45] Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
[00:24.44] Lapilatuu
[00:26.51] Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
[00:28.95] Nyengo yovuta koma osakhulupilira
[00:31.30] Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
[00:33.58] Koma jah jah sazakukhulupilira
[00:35.97] Akufa adzauka, Kaya osauka
[00:38.38] Kaya wachithumba Kaya unali otchuka
[00:40.44] Tidzaona misonzi
[00:42.58] Panzerepo limodzi
[00:44.42] Yeah adzati
[00:46.05] Mfana ndakupatsa Zima chance
[00:47.66] Lero nde palibe zama story
[00:50.21] Mulungu nde salandira Benz
[00:52.75] Palibe zoti kuseri ukamukhole
[00:54.85] Kaya uli ndi ma doller or rands
[00:57.23] Tsiku lomaliza lokha iwe sorry
[00:59.38] Palibe zoti Kaya unali ndima fans
[01:01.74] Panzere udzakhalapo wekha usaitole
[01:05.79] Nde bwanj umachimwabe mulungu ndiwabwno koma osamuyesa
[01:09.92] Ngati ufuna kululumuka ukaona tchimo kumaziletsa
[01:13.64] Kuyesa angel Michael akuti "no"
[01:15.28] Kuyesera king Davide akut "no way"
[01:17.85] Ngat uli ochimwa palibe njira ina
[01:19.93] Tsiku lomaliza kumwambako usakalowe
[01:21.53] Haah
[01:21.68] Tsiku lobwera yesu
[01:24.05] Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
[01:30.35] Tsiku lobwera yesu
[01:33.07] Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
[01:37.52] Lapilatuu
[01:39.91] Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
[01:42.01] Nyengo yovuta koma osakhulupilira
[01:44.44] Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
[01:46.86] Koma jah jah sazakukhulupilira
[01:48.92] Akufa adzauka, Kaya osauka
[01:51.32] Kaya wachithumba Kaya unali otchuka
[01:53.43] Tidzaona misonzi
[01:55.71] Panzerepo limodzi
[01:58.17] Iwe
[01:59.72] Amakupatsa chilichonse chomwe umafuna
[02:01.83] Nanga bwanj ulemu osampatsa
[02:03.93] Ndizija amakulanda chilichonse, akaona akakupatsa iwe umatasa
[02:08.48] Ndeno ma man mutha kulapa kuyisintha nkhani
[02:12.96] Satana mdani, ukapusa akuika pa mpani
[02:17.20] Azaliza lipenga
[02:18.44] Tsiku lomwe lokha mphwanga palibe kuzemba
[02:21.69] Azaliza lipenga
[02:22.77] Alibe nazo ntchito zoti iwe umafalitsa uthenga
[02:26.48] Kaya iwe uma trender
[02:28.08] Kaya doctor umachiritsa matenda
[02:29.80] Kaya fans ikakuona imapanga
[02:32.03] Tsiku lomaliza ndila namalenga
[02:34.47] Tsiku lobwera yesu
[02:37.36] Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
[02:43.46] Tsiku lobwera yesu
[02:45.71] Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
[02:50.54] Lapilatuu
[02:52.92] Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
[02:55.37] Nyengo yovuta koma osakhulupilira
[02:57.41] Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
[02:59.85] Koma jah jah sazakukhulupilira
[03:02.28] Akufa adzauka, Kaya osauka
[03:04.33] Kaya wachithumba Kaya unali otchuka
[03:06.59] Tidzaona misonzi
[03:08.65] Panzerepo limodzi
[03:10.26]