Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Amuna ndi Agalu

๐Ÿ‘ค Henry Czar โ€ข ๐ŸŽผ Amuna ndi Agalu โ€ข โฑ๏ธ 3:19
๐ŸŽต 2275 characters
โฑ๏ธ 3:19 duration
๐Ÿ†” ID: 15052348

๐Ÿ“œ Lyrics

Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dododo
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are do do do

Ndimafuna mamuna wabho
Wa ma lux owoneka bho
Osanyasa ngati akudya mandimu
Six pack adzivaya gym
Adzitchena ngati akakwela ndege
Woti azimzanga asamandiseke
Azindipanga support ngati jeke
Oteleyo nde sindingamuleke
Mamuna adzikhalangati wa zee world
Ozitsata chikondi adzichidziwa
Adzikunyengelela ukakwiya
Bea please am sorry ndasiya
Akhale ovaya heavy akhale ndi Money ne ne
Akhale ndi galimoto iliyonse kaya ndi Benenene
Please call pompo adziyimba phone
Sindikufuna mamuna wangati John
Anangondivulavula mkunditaya
Kundibulabula mkundiponya kumtaya
Anangonditupitsa mkubanduka
Anangondiphulitsa ndi Bazuka
Amuna ndi agalu samaseka amaluma ukapusa amakupanga Geoffrey

Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dododo
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are do do do

Ndimabwera ndi chi bodza kuti
Pa ukwati dzakuveka velo komaso ndidzatchena suit
Pasi pake dzavala sapato yokwiya ankle Buti
Kenako waku photo shoot
Kundipanga trust ndikulola
Posapanga invest ndikolola
Sakudziwa mene wandiputa ine
Ndine Ronaldinho ndimadodadada
Amabwera pa deni atatchena mmaso mwake ataphodadada
Amayesetsa kuchengetela
Koma sindisiya kutchetchelela
Mkazi wachimbina kupemelela
Nde choncho sindisekelela
Ndendende ma girls eti
Mudziwonetsetsa ofuna kupanga date
Amuna ndi agalu amafuna kutsitsa weight
Kenako kukutaya toilet
Ana ena amakhala opanda bambo
Chifukwa chosakhala ndi chisakho
Osatengeka ndi Jumbo Rambo
Kapena usipa micheni ndi chambo

Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dododo
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are do do do

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:24.56] Amuna ndi agalu huuuuu
[00:26.74] Men are dogs
[00:28.36] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[00:29.81] Men are dododo
[00:31.76] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[00:33.88] Men are dogs
[00:35.66] Amuna ndi agalu huuu huuu
[00:37.96] Men are do do do
[00:38.73] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[00:40.14] Men are dogs
[00:42.40] Amuna ndi agalu huuu huuu
[00:44.68] Men are do do do
[00:46.04] Amuna ndi agalu huuuuu
[00:48.19] Men are dogs
[00:49.53] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[00:51.78] Men are do do do
[00:53.01] Ndimafuna mamuna wabho
[00:54.76] Wa ma lux owoneka bho
[00:56.65] Osanyasa ngati akudya mandimu
[00:58.36] Six pack adzivaya gym
[01:00.12] Adzitchena ngati akakwela ndege
[01:02.05] Woti azimzanga asamandiseke
[01:03.73] Azindipanga support ngati jeke
[01:05.52] Oteleyo nde sindingamuleke
[01:07.35] Mamuna adzikhalangati wa zee world
[01:09.20] Ozitsata chikondi adzichidziwa
[01:11.00] Adzikunyengelela ukakwiya
[01:12.71] Bea please am sorry ndasiya
[01:14.62] Akhale ovaya heavy akhale ndi Money ne ne
[01:18.43] Akhale ndi galimoto iliyonse kaya ndi Benenene
[01:21.99] Please call pompo adziyimba phone
[01:23.78] Sindikufuna mamuna wangati John
[01:25.57] Anangondivulavula mkunditaya
[01:27.05] Kundibulabula mkundiponya kumtaya
[01:29.10] Anangonditupitsa mkubanduka
[01:30.83] Anangondiphulitsa ndi Bazuka
[01:32.54] Amuna ndi agalu samaseka amaluma ukapusa amakupanga Geoffrey
[01:36.16] Amuna ndi agalu huuuuu
[01:38.19] Men are dogs
[01:39.78] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[01:41.80] Men are dododo
[01:43.49] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[01:45.46] Men are dogs
[01:46.84] Amuna ndi agalu huuu huuu
[01:49.19] Men are do do do
[01:50.49] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[01:52.53] Men are dogs
[01:54.00] Amuna ndi agalu huuu huuu
[01:56.36] Men are do do do
[01:57.79] Amuna ndi agalu huuuuu
[01:59.87] Men are dogs
[02:01.29] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[02:03.34] Men are do do do
[02:04.60] Ndimabwera ndi chi bodza kuti
[02:06.81] Pa ukwati dzakuveka velo komaso ndidzatchena suit
[02:10.19] Pasi pake dzavala sapato yokwiya ankle Buti
[02:13.61] Kenako waku photo shoot
[02:15.52] Kundipanga trust ndikulola
[02:17.30] Posapanga invest ndikolola
[02:19.13] Sakudziwa mene wandiputa ine
[02:21.05] Ndine Ronaldinho ndimadodadada
[02:23.50] Amabwera pa deni atatchena mmaso mwake ataphodadada
[02:27.12] Amayesetsa kuchengetela
[02:28.83] Koma sindisiya kutchetchelela
[02:30.45] Mkazi wachimbina kupemelela
[02:32.13] Nde choncho sindisekelela
[02:33.96] Ndendende ma girls eti
[02:36.20] Mudziwonetsetsa ofuna kupanga date
[02:37.99] Amuna ndi agalu amafuna kutsitsa weight
[02:39.75] Kenako kukutaya toilet
[02:41.58] Ana ena amakhala opanda bambo
[02:43.39] Chifukwa chosakhala ndi chisakho
[02:45.25] Osatengeka ndi Jumbo Rambo
[02:46.94] Kapena usipa micheni ndi chambo
[02:47.94] Amuna ndi agalu huuuuu
[02:49.84] Men are dogs
[02:51.44] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[02:53.58] Men are dododo
[02:55.04] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[02:57.11] Men are dogs
[02:58.47] Amuna ndi agalu huuu huuu
[03:00.72] Men are do do do
[03:02.02] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[03:04.14] Men are dogs
[03:05.66] Amuna ndi agalu huuu huuu
[03:07.87] Men are do do do
[03:09.39] Amuna ndi agalu huuuuu
[03:11.38] Men are dogs
[03:12.92] Amuna ndi agalu uhuuuuu
[03:14.92] Men are do do do
[03:16.48]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings