Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Mtundu Wanga Ndisiye

๐Ÿ‘ค Billy Kaunda โ€ข ๐ŸŽผ Mwataya Chipangano (Agalatia) โ€ข โฑ๏ธ 5:55
๐ŸŽต 1326 characters
โฑ๏ธ 5:55 duration
๐Ÿ†” ID: 15111442

๐Ÿ“œ Lyrics

Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah

Mayo ndakulakwiranji iwe?
Mayo bwenzi lokondeka iwe
Mayo mtima ukuwawa bwanji iwe?
Mayo ndiyankhe tsopanoli iwe
Mtundu wanga, mtundu wanga iwe
Ndakulakwitra chani iwe?
Kuti mpakana undiphe iwe
Panalibe chilango china kodi iwe?
Chomwe ukanandipatsa ine

Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah

Kodi ndine woyamba iwe?
Kuti ndikulakwire iwe
Sindinayembekezele iwe
Kuti mpaka ungandiphe iwe
Ndisanakaweluzidwe ine

Mayo wandipha ngati njoka ine
Mayo kodi umapemphera iwe?
Mayo kuyesa kufuula ine
Mayo osamva chisoni iwe
Pomwe umkandigwira iwe
Sindinafune kuthawa ine
Poti ndinali kudziwa ine
Kuti ndiwe mtundu wanga iwe
Tikakambirana zizatha iwe
Mayo kundimenya njira yonse iwe
Mayo pomangidwa mikono ine
Mayo tunthu wanga ndisiye iwe
Mayo ndafa imfa ya njoka ine

.Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah

.Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:41.45] Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[00:48.29] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[00:54.72] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[01:01.66] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[01:07.77] Mayo ndakulakwiranji iwe?
[01:14.46] Mayo bwenzi lokondeka iwe
[01:20.97] Mayo mtima ukuwawa bwanji iwe?
[01:27.80] Mayo ndiyankhe tsopanoli iwe
[01:34.27] Mtundu wanga, mtundu wanga iwe
[01:40.73] Ndakulakwitra chani iwe?
[01:47.60] Kuti mpakana undiphe iwe
[01:54.17] Panalibe chilango china kodi iwe?
[02:00.85] Chomwe ukanandipatsa ine
[02:21.82] Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[02:28.40] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[02:35.15] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[02:41.61] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[02:47.67] Kodi ndine woyamba iwe?
[02:54.31] Kuti ndikulakwire iwe
[03:00.96] Sindinayembekezele iwe
[03:07.68] Kuti mpaka ungandiphe iwe
[03:14.19] Ndisanakaweluzidwe ine
[03:21.37] Mayo wandipha ngati njoka ine
[03:27.80] Mayo kodi umapemphera iwe?
[03:34.43] Mayo kuyesa kufuula ine
[03:41.21] Mayo osamva chisoni iwe
[04:01.01] Pomwe umkandigwira iwe
[04:07.68] Sindinafune kuthawa ine
[04:14.20] Poti ndinali kudziwa ine
[04:21.15] Kuti ndiwe mtundu wanga iwe
[04:27.75] Tikakambirana zizatha iwe
[04:34.45] Mayo kundimenya njira yonse iwe
[04:40.85] Mayo pomangidwa mikono ine
[04:47.58] Mayo tunthu wanga ndisiye iwe
[04:54.12] Mayo ndafa imfa ya njoka ine
[05:01.32] .Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[05:08.03] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[05:14.68] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[05:21.34] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[05:27.90] .Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[05:34.52] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[05:41.43] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[05:47.88] Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
[05:53.87]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings