Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Wanga Kheliwe

๐Ÿ‘ค Lucius Banda โ€ข ๐ŸŽผ Fifteen Fifteen โ€ข โฑ๏ธ 3:55
๐ŸŽต 1526 characters
โฑ๏ธ 3:55 duration
๐Ÿ†” ID: 15192990

๐Ÿ“œ Lyrics

Nditakhala pa mchenga
Woyera ku Salima
Nkhwazi kuwuluka
Ndidaona nyenyezi
Nditasokhanitsa mphamvu
Kumukodola nkumuyankhula
Lero mam'mawa ndamuveka mphete uyu
Ndiwanga Kheliwe

Oh wanga Kheliwe
Ndiwe wanga Kheliwe
Ndiwe wanga Kheliwe
Tidzakondane Kheliwe
Ndiwe wanga Kheliwe
Ndiwe wanga Kheliwe
Ndiwe wanga Kheliwe
Tidzakondane Kheliwe

Ndzakukonda Kheliwe
M'moyo wanga wonse
Pamtendere pa mavuto Kheliwe
Ndzakukonda Kheliwe
M'moyo wanga wonse
Pamtendere pa mavuto Kheliwe

Mkazi wokongola
Woyiwalitsa mavuto
Ndayenda m'dziko lonse
Ndagonjera pa iwe
Ukamaseka ngati sukufuna
Ukamayenda ngati ukuvina
Ukavale mphete ya golide Kheliwe

Kheliwe eeh, wanga Kheliwe
Kheliwe, ndiwe wanga Kheliwe
Kheliwe, ndiwe wanga kheliwe
Tidzakondane Kheliwe
Mkazi wanga Kheliwe, ndiwe wanga Kheliwe
Mkazi wanga Kheliwe, ndiwe wanga Kheliwe
Kheliwe, ndiwe wanga Kheliwe
Tizakondane Kheliwe (Kheliwe)

Tandigwire kudzanja Kheliwe
Tipite ku guwa Kheliwe
Ukavale mphete ya golide Kheliwe
Nthawi zonse limodzi Kheliwe
Mkazi wanga Kheliwe
Ona makolo akululuta kukondwa
Ukwati woyera Kheliwe

Ngati wandikonda ukafike kwathu
Ngati wandikonda undiveke mphete
Ngati wandikonda undiveke vero
Tidzakondane honey
Ngati wandikonda ukafike kwathu
Ngati wandikonda undiveke mphete
Ngati wandikonda undiveke vero
Tidzasungane Daka

Ngati wandikonda ukafike kwathu
Ngati wandikonda undiveke mphete
Ngati wandikonda undiveke vero
Tidzakondane honey
Ngati wandikonda ukafike kwathu
Ngati wandikonda undiveke mphete
Ngati wandikonda undiveke vero
Tidzasungane honey

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:43.81] Nditakhala pa mchenga
[00:46.57] Woyera ku Salima
[00:48.82] Nkhwazi kuwuluka
[00:51.73] Ndidaona nyenyezi
[00:54.33] Nditasokhanitsa mphamvu
[00:56.78] Kumukodola nkumuyankhula
[00:59.25] Lero mam'mawa ndamuveka mphete uyu
[01:02.29] Ndiwanga Kheliwe
[01:03.94] Oh wanga Kheliwe
[01:06.90] Ndiwe wanga Kheliwe
[01:09.47] Ndiwe wanga Kheliwe
[01:11.88] Tidzakondane Kheliwe
[01:14.98] Ndiwe wanga Kheliwe
[01:17.51] Ndiwe wanga Kheliwe
[01:19.94] Ndiwe wanga Kheliwe
[01:22.77] Tidzakondane Kheliwe
[01:25.46] Ndzakukonda Kheliwe
[01:27.76] M'moyo wanga wonse
[01:30.31] Pamtendere pa mavuto Kheliwe
[01:35.74] Ndzakukonda Kheliwe
[01:38.42] M'moyo wanga wonse
[01:40.77] Pamtendere pa mavuto Kheliwe
[01:43.92]
[01:46.71] Mkazi wokongola
[01:49.25] Woyiwalitsa mavuto
[01:51.78] Ndayenda m'dziko lonse
[01:53.73] Ndagonjera pa iwe
[01:56.99] Ukamaseka ngati sukufuna
[01:59.55] Ukamayenda ngati ukuvina
[02:02.36] Ukavale mphete ya golide Kheliwe
[02:06.01] Kheliwe eeh, wanga Kheliwe
[02:08.48] Kheliwe, ndiwe wanga Kheliwe
[02:11.37] Kheliwe, ndiwe wanga kheliwe
[02:14.59] Tidzakondane Kheliwe
[02:16.51] Mkazi wanga Kheliwe, ndiwe wanga Kheliwe
[02:19.30] Mkazi wanga Kheliwe, ndiwe wanga Kheliwe
[02:23.02] Kheliwe, ndiwe wanga Kheliwe
[02:25.29] Tizakondane Kheliwe (Kheliwe)
[02:28.46] Tandigwire kudzanja Kheliwe
[02:31.12] Tipite ku guwa Kheliwe
[02:33.34] Ukavale mphete ya golide Kheliwe
[02:38.85] Nthawi zonse limodzi Kheliwe
[02:41.50] Mkazi wanga Kheliwe
[02:43.51] Ona makolo akululuta kukondwa
[02:45.84] Ukwati woyera Kheliwe
[02:49.94]
[03:09.90] Ngati wandikonda ukafike kwathu
[03:12.54] Ngati wandikonda undiveke mphete
[03:14.92] Ngati wandikonda undiveke vero
[03:17.17] Tidzakondane honey
[03:20.21] Ngati wandikonda ukafike kwathu
[03:22.73] Ngati wandikonda undiveke mphete
[03:25.32] Ngati wandikonda undiveke vero
[03:27.63] Tidzasungane Daka
[03:30.61] Ngati wandikonda ukafike kwathu
[03:33.24] Ngati wandikonda undiveke mphete
[03:35.78] Ngati wandikonda undiveke vero
[03:38.10] Tidzakondane honey
[03:40.98] Ngati wandikonda ukafike kwathu
[03:43.68] Ngati wandikonda undiveke mphete
[03:46.05] Ngati wandikonda undiveke vero
[03:48.44] Tidzasungane honey
[03:52.39]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings