Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Umpeze Wina

๐Ÿ‘ค Maskal โ€ข ๐ŸŽผ Umunthu โ€ข โฑ๏ธ 3:28
๐ŸŽต 1690 characters
โฑ๏ธ 3:28 duration
๐Ÿ†” ID: 15193013

๐Ÿ“œ Lyrics

(Woti udzimunamiza)
(Yemwe uzimupusitsa)
(Kukupatsa chikondi)
(Umpeze wina)

Wakhala ukundinamiza
Ndinakupatsa mwayi omaliza
Lero wapanganso chimodzimodzi
Ndatopa, ndatopa
Ndiwe munthu wa mtundu wanji?
Kunamiza munthu umamva bwanji?
Ndinayesa kupeleka chikondi
Ndatopa, ndatopa

Chikondi chomwe n'napeleka kwa Iwe
Ndichomwe chinatsala mtima mwa Ine
Sindingakwanitse kukhala ndi Iwe
Ndapita, ndapita

Umpeze wina, woti udzimunamiza
Umpeze wina, yemwe uzimupusitsa
N'nayesetsa kukakamira
Kukupatsa chikondi
Ndakanika, mupeze wina

Ndili ndi mantha Ine
Ndikakupatsa mwayi wina Iwe
Ndikupatsa chipolopolo poti unandiphonya poyamba paja
I thought I was part of your life
I thought you'll be my wife
Kukhaka mchikondi ndi zomwe mtima wanga umkafuna

Chikondi chomwe nnapeleka kwa Iwe
Ndichomwe chinatsala mtima mwa Ine
Sindingakwanitse kukhala ndi Iwe
Ndapita, Ndapita

Umpeze wina, woti udzimunamiza (ndapita baby)
Umpeze wina, yemwe uzimupusitsa (oh oh oh oh)
N'nayesetsa kukakamira (n'nayesetsa kukakamira)
Kukupatsa chikondi (ndakanika baby)
Ndakanika, mupeze wina (eh eh oh)

Love was all I wanted
Love was all I needed
I don't know what you gave me
I don't know why
Chikondi chomwe nnapeleka kwa Iwe
Ndichomwe chinatsala mtima mwa Ine
Sindingakwanitse kukhala ndi Iwe
Ndapita, Ndapita

Umpeze wina, woti udzimunamiza
Umpeze wina, yemwe uzimupusitsa
N'nayesetsa kukakamira (n'nayesetsa kukakamira)
Kukupatsa chikondi (kukupatsa chikondi baby)
Ndakanika, mupeze wina (eh oh)

Umpeze wina, woti udzimunamiza
Umpeze wina, yemwe uzimupusitsa (yeah, yeah-eh-eh-eh)
N'nayesetsa kukakamira (n'nayesetsa kukakamira)
Kukupatsa chikondi (n'nayesetsa kukakamira)
Ndakanika, mupeze wina (ndakanika baby)

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:01.88] (Woti udzimunamiza)
[00:07.40] (Yemwe uzimupusitsa)
[00:13.39] (Kukupatsa chikondi)
[00:19.56] (Umpeze wina)
[00:23.34] Wakhala ukundinamiza
[00:26.19] Ndinakupatsa mwayi omaliza
[00:29.19] Lero wapanganso chimodzimodzi
[00:32.03] Ndatopa, ndatopa
[00:34.20] Ndiwe munthu wa mtundu wanji?
[00:37.76] Kunamiza munthu umamva bwanji?
[00:40.49] Ndinayesa kupeleka chikondi
[00:43.27] Ndatopa, ndatopa
[00:46.09] Chikondi chomwe n'napeleka kwa Iwe
[00:48.74] Ndichomwe chinatsala mtima mwa Ine
[00:51.50] Sindingakwanitse kukhala ndi Iwe
[00:54.31] Ndapita, ndapita
[00:56.39] Umpeze wina, woti udzimunamiza
[01:01.91] Umpeze wina, yemwe uzimupusitsa
[01:06.92] N'nayesetsa kukakamira
[01:09.70] Kukupatsa chikondi
[01:13.03] Ndakanika, mupeze wina
[01:18.45] Ndili ndi mantha Ine
[01:20.80] Ndikakupatsa mwayi wina Iwe
[01:23.52] Ndikupatsa chipolopolo poti unandiphonya poyamba paja
[01:30.92] I thought I was part of your life
[01:33.85] I thought you'll be my wife
[01:36.42] Kukhaka mchikondi ndi zomwe mtima wanga umkafuna
[01:42.66] Chikondi chomwe nnapeleka kwa Iwe
[01:45.20] Ndichomwe chinatsala mtima mwa Ine
[01:48.09] Sindingakwanitse kukhala ndi Iwe
[01:50.95] Ndapita, Ndapita
[01:52.78] Umpeze wina, woti udzimunamiza (ndapita baby)
[01:58.59] Umpeze wina, yemwe uzimupusitsa (oh oh oh oh)
[02:03.55] N'nayesetsa kukakamira (n'nayesetsa kukakamira)
[02:06.14] Kukupatsa chikondi (ndakanika baby)
[02:10.04] Ndakanika, mupeze wina (eh eh oh)
[02:16.54] Love was all I wanted
[02:19.34] Love was all I needed
[02:22.18] I don't know what you gave me
[02:25.84] I don't know why
[02:27.91] Chikondi chomwe nnapeleka kwa Iwe
[02:30.57] Ndichomwe chinatsala mtima mwa Ine
[02:33.43] Sindingakwanitse kukhala ndi Iwe
[02:36.02] Ndapita, Ndapita
[02:38.24] Umpeze wina, woti udzimunamiza
[02:43.66] Umpeze wina, yemwe uzimupusitsa
[02:48.77] N'nayesetsa kukakamira (n'nayesetsa kukakamira)
[02:51.49] Kukupatsa chikondi (kukupatsa chikondi baby)
[02:54.98] Ndakanika, mupeze wina (eh oh)
[03:00.72] Umpeze wina, woti udzimunamiza
[03:05.92] Umpeze wina, yemwe uzimupusitsa (yeah, yeah-eh-eh-eh)
[03:11.38] N'nayesetsa kukakamira (n'nayesetsa kukakamira)
[03:14.28] Kukupatsa chikondi (n'nayesetsa kukakamira)
[03:17.60] Ndakanika, mupeze wina (ndakanika baby)
[03:25.80]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings