Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Akuzike

๐Ÿ‘ค Mic Mash โ€ข ๐ŸŽผ Akuzike โ€ข โฑ๏ธ 3:20
๐ŸŽต 1718 characters
โฑ๏ธ 3:20 duration
๐Ÿ†” ID: 15260201

๐Ÿ“œ Lyrics

Ey
Ambuye
Mwandichotsa kutali
Olo nditani matengabe yanga mbali
Sindingakutayeni ntakhala millionaire
Moyo ndi wanu mumatipatsa million air
Mpweya waulele
Moyo waulele
Munatumiza mwana wanu kuti azandifele
Alipo ena akuvutika muchipatala
Ndi chibwana chabe chosakonda church koma bara
Mwandikondera
Ndiye ndikuti zikomo
Ndikukondeni mu mtendere ndimuzikhomo
No lorry kodi yesuyo wantani?
Kuti akudalitseni motere man
Nthawi zambiri nkamawelenga madalitso is wealth
Ndimaiwala zinthu ngati good health
Ambuye akuzike
You make me win battles that I cannot see ngati ine Baba Vos

Mwayenera
Ulemu mwayenera
Pomwe ndimalephera
Tate mumandigwila dzanja
Mbuye wanga you give everything
More than I've ever needed
Muzonse ndidutsamo
Nyimbo yanga ndi
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike Yahwe
Yeah
Atamandike atamandike
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike Yahwe

Munandithyolera nde nde siza Paulo ndi Sirah basi
Mwana wa atate nde sindingasinthe syllabus
Ndisinthe ndilalike za mudziko?
Haaaa iweee!!
Moyo ndi wake nde ndimukwezeke Yahweh
Akuzike
Munadalitsa kupanga kuti malire akuzike
Mwandipatsa zofunika komanso chimoyo cha thanzi
Simphamvu zanga kupeza zonsezi
Opanda inu sindingayesele olo wezi
Mwandikweza kuchoka pa Mira pano pa Benz
Kundidziwa nsanabadwe and you know the number of my days
Athu ndi mapulani inu makhazikitsa
Muli nafe pulani inu simulakwitsa
Nzeru ndikulimbika inu munatipatsa
Mundikweze pomwe adani afuna kunditsitsa

Mwayenera
Ulemu mwayenera
Pomwe ndimalephera
Tate mumandigwila dzanja
Ooh you give everything
More than I ever needed
Muzonse ndidutsamo
Nyimbo yanga ndi
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike Yahwe
Yeah
Atamandike atamandike
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike Yahwe

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:19.54] Ey
[00:20.79] Ambuye
[00:22.52] Mwandichotsa kutali
[00:24.36] Olo nditani matengabe yanga mbali
[00:26.66] Sindingakutayeni ntakhala millionaire
[00:29.37] Moyo ndi wanu mumatipatsa million air
[00:31.93] Mpweya waulele
[00:33.06] Moyo waulele
[00:34.53] Munatumiza mwana wanu kuti azandifele
[00:36.92] Alipo ena akuvutika muchipatala
[00:39.34] Ndi chibwana chabe chosakonda church koma bara
[00:42.41] Mwandikondera
[00:43.90] Ndiye ndikuti zikomo
[00:45.62] Ndikukondeni mu mtendere ndimuzikhomo
[00:48.32] No lorry kodi yesuyo wantani?
[00:50.63] Kuti akudalitseni motere man
[00:53.69] Nthawi zambiri nkamawelenga madalitso is wealth
[00:56.69] Ndimaiwala zinthu ngati good health
[00:59.27] Ambuye akuzike
[01:00.45] You make me win battles that I cannot see ngati ine Baba Vos
[01:03.90] Mwayenera
[01:05.73] Ulemu mwayenera
[01:08.44] Pomwe ndimalephera
[01:11.47] Tate mumandigwila dzanja
[01:13.80] Mbuye wanga you give everything
[01:17.09] More than I've ever needed
[01:19.70] Muzonse ndidutsamo
[01:22.40] Nyimbo yanga ndi
[01:24.36] Akuzike akuzike
[01:27.05] Akuzike akuzike
[01:29.80] Akuzike akuzike Yahwe
[01:33.99] Yeah
[01:35.14] Atamandike atamandike
[01:37.70] Akuzike akuzike
[01:40.47] Akuzike akuzike Yahwe
[01:45.49] Munandithyolera nde nde siza Paulo ndi Sirah basi
[01:49.38] Mwana wa atate nde sindingasinthe syllabus
[01:52.39] Ndisinthe ndilalike za mudziko?
[01:54.04] Haaaa iweee!!
[01:54.90] Moyo ndi wake nde ndimukwezeke Yahweh
[01:57.01] Akuzike
[02:00.40] Munadalitsa kupanga kuti malire akuzike
[02:05.61] Mwandipatsa zofunika komanso chimoyo cha thanzi
[02:08.53] Simphamvu zanga kupeza zonsezi
[02:10.51] Opanda inu sindingayesele olo wezi
[02:13.14] Mwandikweza kuchoka pa Mira pano pa Benz
[02:15.85] Kundidziwa nsanabadwe and you know the number of my days
[02:19.00] Athu ndi mapulani inu makhazikitsa
[02:21.73] Muli nafe pulani inu simulakwitsa
[02:24.32] Nzeru ndikulimbika inu munatipatsa
[02:26.65] Mundikweze pomwe adani afuna kunditsitsa
[02:29.03] Mwayenera
[02:31.16] Ulemu mwayenera
[02:33.71] Pomwe ndimalephera
[02:36.50] Tate mumandigwila dzanja
[02:39.05] Ooh you give everything
[02:42.38] More than I ever needed
[02:44.99] Muzonse ndidutsamo
[02:47.66] Nyimbo yanga ndi
[02:49.74] Akuzike akuzike
[02:52.44] Akuzike akuzike
[02:55.04] Akuzike akuzike Yahwe
[02:59.54] Yeah
[03:00.49] Atamandike atamandike
[03:03.04] Akuzike akuzike
[03:05.72] Akuzike akuzike Yahwe
[03:12.07]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings