Home ๐ŸŽฌ Bollywood ๐ŸŽต Pakistani ๐ŸŽค English Pop

Mabala

๐Ÿ‘ค Lucius Banda โ€ข ๐ŸŽผ Son of the Poor Man โ€ข โฑ๏ธ 4:36
๐ŸŽต 1904 characters
โฑ๏ธ 4:36 duration
๐Ÿ†” ID: 16386076

๐Ÿ“œ Lyrics

Panali anthu ena wongovutika
Pamene anthu ena amkangokondwera
Panalia anthu ena wogwira ntchito
Pamene anthu ena amkangodyelera
Malume ndalama kubisa ku bank
Pamene mbumba yanu ikufa ndi njala
Koma zowuluka zonse zitawuluka
Pali tsiku limodzi zitadzatele

Inu mumati zidzakhala choncho
Mpaka liti abale?
Ana a Mulungu sangakhale akulira
Masiku onse a moyo wawo
Analanda ufumu kalero
Nawupeleka kwa woyenera
Ndichani chingamulake
Mbuye Mulungu wachilungamo!
Ndi wachikondi

Tsiku la Mulungu ndi lopambana
Koma linali tsiku la masewera
Amayi kulephera kusunga banja
Koma Ambuye sanakondwere nazo
Anthu anzeru opempha chilungamo
Amkangofa monga muja zifera ntchetche
Koma zowuluka zonse zitawuluka
Pali tsiku limodzi zitadzatele

Inu mumati zidzakhala choncho
Mpaka liti abale?
Ana a Mulungu sangakhale akulira
Masiku onse a moyo wawo
Analanda ufumu kalero
Nawupeleka kwa woyenera
Ndichani chingamulake
Mbuye Mulungu wachilungamo!
Ndi wachikondi

Ukhululuke iwe nzanga ofedwa
Puputa misozi tiyiwale zonse
Nyali yawala nkhuku ija yathawa
Tisangalare poti Mbuye watikumbuka
Zokulipa diso izo siyani
Zikanatero bwezi tonse tili a khungu
Kukhululuka ndiye ndakhululuka
Koma mabalawa ndiye akupweteka

Inu mumati zidzakhala choncho
Mpaka liti abale?
Ana a Mulungu sangakhale akulira
Masiku onse a moyo wawo
Analanda ufumu kalero
Nawupeleka kwa woyenera
Ndichani chingamulake
Mbuye Mulungu wachilungamo!

Inu mumati zidzakhala choncho
Mpaka liti abale?
Ana a Mulungu sangakhale akulira
Masiku onse a moyo wawo
Analanda ufumu kalero
Nawupeleka kwa woyenera
Ndichani chingamulake
Mbuye Mulungu wachilungamo!

Inu mumati zidzakhala choncho
Mpaka liti abale?
Ana a Mulungu sangakhale akulira
Masiku onse a moyo wawo
Analanda ufumu kalero
Nawupeleka kwa woyenera
Ndichani chingamulake
Mbuye Mulungu wachilungamo!

Inu mumati zidzakhala choncho
Mpaka liti abale?
Ana a Mulungu sangakhale akulira
Masiku onse a moyo wawo

โฑ๏ธ Synced Lyrics

[00:29.48] Panali anthu ena wongovutika
[00:32.37] Pamene anthu ena amkangokondwera
[00:35.46] Panalia anthu ena wogwira ntchito
[00:38.27] Pamene anthu ena amkangodyelera
[00:41.46] Malume ndalama kubisa ku bank
[00:44.42] Pamene mbumba yanu ikufa ndi njala
[00:47.21] Koma zowuluka zonse zitawuluka
[00:50.05] Pali tsiku limodzi zitadzatele
[00:52.64] Inu mumati zidzakhala choncho
[00:55.78] Mpaka liti abale?
[00:59.25] Ana a Mulungu sangakhale akulira
[01:01.89] Masiku onse a moyo wawo
[01:05.32] Analanda ufumu kalero
[01:08.08] Nawupeleka kwa woyenera
[01:11.43] Ndichani chingamulake
[01:14.08] Mbuye Mulungu wachilungamo!
[01:19.35] Ndi wachikondi
[01:21.75]
[01:32.23] Tsiku la Mulungu ndi lopambana
[01:34.97] Koma linali tsiku la masewera
[01:38.17] Amayi kulephera kusunga banja
[01:41.05] Koma Ambuye sanakondwere nazo
[01:44.26] Anthu anzeru opempha chilungamo
[01:46.86] Amkangofa monga muja zifera ntchetche
[01:49.85] Koma zowuluka zonse zitawuluka
[01:52.46] Pali tsiku limodzi zitadzatele
[01:55.62] Inu mumati zidzakhala choncho
[01:58.49] Mpaka liti abale?
[02:01.73] Ana a Mulungu sangakhale akulira
[02:04.45] Masiku onse a moyo wawo
[02:07.64] Analanda ufumu kalero
[02:10.38] Nawupeleka kwa woyenera
[02:13.73] Ndichani chingamulake
[02:16.32] Mbuye Mulungu wachilungamo!
[02:22.15] Ndi wachikondi
[02:24.66]
[02:34.60] Ukhululuke iwe nzanga ofedwa
[02:37.18] Puputa misozi tiyiwale zonse
[02:40.57] Nyali yawala nkhuku ija yathawa
[02:43.23] Tisangalare poti Mbuye watikumbuka
[02:46.53] Zokulipa diso izo siyani
[02:49.52] Zikanatero bwezi tonse tili a khungu
[02:52.71] Kukhululuka ndiye ndakhululuka
[02:55.19] Koma mabalawa ndiye akupweteka
[02:58.11] Inu mumati zidzakhala choncho
[03:01.33] Mpaka liti abale?
[03:04.57] Ana a Mulungu sangakhale akulira
[03:07.15] Masiku onse a moyo wawo
[03:10.42] Analanda ufumu kalero
[03:13.02] Nawupeleka kwa woyenera
[03:16.28] Ndichani chingamulake
[03:18.99] Mbuye Mulungu wachilungamo!
[03:25.10] Inu mumati zidzakhala choncho
[03:28.03] Mpaka liti abale?
[03:31.26] Ana a Mulungu sangakhale akulira
[03:33.86] Masiku onse a moyo wawo
[03:37.39] Analanda ufumu kalero
[03:39.72] Nawupeleka kwa woyenera
[03:43.08] Ndichani chingamulake
[03:45.98] Mbuye Mulungu wachilungamo!
[03:51.96] Inu mumati zidzakhala choncho
[03:54.93] Mpaka liti abale?
[03:58.13] Ana a Mulungu sangakhale akulira
[04:00.94] Masiku onse a moyo wawo
[04:04.07] Analanda ufumu kalero
[04:06.75] Nawupeleka kwa woyenera
[04:10.19] Ndichani chingamulake
[04:12.78] Mbuye Mulungu wachilungamo!
[04:18.54] Inu mumati zidzakhala choncho
[04:21.46] Mpaka liti abale?
[04:24.80] Ana a Mulungu sangakhale akulira
[04:27.67] Masiku onse a moyo wawo
[04:30.98]

โญ Rate These Lyrics

โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†โ˜†
Average: 0.0/5 โ€ข 0 ratings